Bwalo lachinyamata + Malido

#Lido. Kodi inu mutakhala kut mwapeza mkazi or mamuna ndeye apongozi anu akuzen kut apongozi mkazi ndimeneyi koma ndikufuna pofika mawa nyumbamu khale mutabadwa mwana. Ndiye mutakhala inu mungatani kut muwathese zelu apongozi anu?