MY MALAWI ,MY LAND

Peter s speech empty. Akuti katundu akukwela coz of cashgate of k24bn yet JB drove the same boat with cashgate of k92bn mitengo idali boo! Mpaka ma vender a chimanga akulila with availability of maize. Akuti oposition leaders are fueling the strikes yet he was the one ankanena kuti anthu azidzalandila vindalama osati chenje.. Chindoda kuyankhula mopusa kumati opposition is underminhng his goverment in and out of malawi yet JB did not waste time kunena a opposition, she was focusing in uplifting peoples lives. Kudzudzula aku MA COURT akuti boma has no money to increase, bwanji osangotenga zomwe zakanika kudzionjezela zija muwapatse? Why dint he talk of BEAM refund to NAC ndalama zimene adaba getu? Pitala has misd the oportunity.