Malawians in South Africa.

Moni a Malawi nonse muli kuno ku South Africa, Masukani kucheza ndi kudziwana ndi abale ndi alongo onse ali kuno. Tiyeni tikambirane zochitika mdziko lathu, zandale, zamalonda ndi zina zotero. Tiyeni tithandizane kupezerana zinthchito ndi miwayi yina yomwe anthu ena samaipeza.