MALAWIANS IN RSA

Pamene zovuta zakufikilani... pamene m'dani oyipayo wakuzingani... chilichonse sichikuyenda monga mumaganizira... kaya ndi ulova, kusowa banja, mwana, kusalidwa, kunyozedwa, kaya muli pachiphsyinjo chamtundu wanji.... ndikupemphera kuti Yesu Khristu AKUWOLOTSENI nonse nimukakhale mu moyo osangalara. Ngati muli ndi nthawi lembani kuti amen.....