MALAWI POLITICS

This group is about politics in malawi not Religion group weather Muslim or Christian your welcome with your views about politics in our country Malawi.We dont allow any abusive or hurt words here.

C H E N J E Z O

1-Aliyense opeleka ndemanga zosemphana ndi post yomwe yalembedwa kapena kunyoza mzake pa post,adzalandira chenjezo ndipo akamapitiriza kutero adzatulutsidwa mugulumu..

2-Post yonyozerana mitundu kapena zipembedzo idzachotsedwa komanso olembayo adzalandira chenjezo ndipo akamadzapitiliza kulemba adzachotsedwa mugululi..

3-Nkhani zanu zizikhala zoona komanso za umboni,tipewe bodza.

4-Gululi ndilawina aliyense amene ali mmalawi kaya umasapota chipani china chake zilibe kandu chomwe tikufuna ife ndikuwaziwitsa amzathu amene ali kutali mmene ndale zikuyendera kumalawi kuno.

NOTE;Gululi ndi landale silachipembedzo kapena mtundu wina wake ayii!!choncho ndibwino kupanga ndale zokomera wina aliyense..Tikondane ngati ana abanja limodzi la Malawi..Sibwino kumakumbana mitundu kapena zipembedzo kaya zipani...Kaya ndiwe Msilamu,khristu,wamboni,wapuseapuse koma tonse ndife amalawi..Kaya ndiwe wakumpoto,kummwela,pakati,kummawa tonse ndife amalawi..Kaya umasapota UDF,DPP,PP,MCP,AFORD,kaya chatha chija koma tonse ndamalawi tipange ndale zokomera tonse.

Z I K O M O