PABWALO LA NTHABWALA ZA A MALAWI 24HRS KUMVESA KUKOMA!

bengo avuta ndima abbreviation ku ma
interview aulonda!!
Bwana:takulandilani dzina lanu ndani?
Bengo:B.M.W
bwana:kutanthauza?
Bengo:Bengo Mfana Wotchukuma
bwana:mumakhala kuti?
Bengo:K.G
bwana:kutanthauza?
Bengo:Kwa Goliyati!
Bwana:maphunziroanu?
Bengo:N.P
bwana:kutanthauza?
Bengo:Ndinathawila Pawindo!
Bwana:chakupangitsani kuti mufunsile
nchito kuno ndi chani?
Bengo:M.A
bwana:kutanthauza?
Bengo:Mavuto Azachuma
bwana:oky!
Bengo(kufuxa bwana):K.P.Y.I.B?
bwana:kutanthauza chani?
Bengo:Koma Perfomance Yanga Ili Bho?!!
Bwana:N.O.K.M!!
bengo:mukutanthauza?
Bwana:Ndinu Ofunika Ku Mental!!