Malawi's Hottest Soccer Chat.

GULU ili ndila SAPOTA wina aliyense ndipo wa team iliyonse. Zithunzi kapena nkhani zosagwirizana ndi mpira ndizosaloredwa komanso kutsatsa malonda pa gulu ili sizovemerezedwa. Membala osanvera malamulo kapena otukwana adzachotsedwa pa gulupa.

Masukani kulemba nkhani za mpira